Kodi lero mupanga design yotani?
Pangani ndi AI, zolemba za pa ma social media, mavidiyo, ma presentation ndi zambiri pogwiritsa ntchito Canva.
Zida zothandizira kuti ntchito yanu ikhale yabwino
Pititsani patsogolo luso lanu lolemba ndi Magic Write
Gwirani ntchito limodzi ndi mnzanu watsopano pa @Canva
Chotsani ma background a chithunzi ndi vidiyo pongodina kamodzi basi
Tsukani zithunzi ndi Magic Erase
Pangani design ndi ma tempuleti ochititsa chidwi
Tsukani zithunzi ndi Magic Erase
Chotsani ma background a chithunzi ndi vidiyo pongodina kamodzi basi
Sinthani saizi ya ma design mwachangu omwe angagwiritsidwe ntchito pa tchanelo iliyonse
Sangalatsani anthu omwe amakonda zinthu zanu pogwiritsa ntchito zithunzi ndi mavidiyo atsopano
Pezani ma tempuleti opangidwa mogwirizana ndi ndi nyimbo
Chotsani ma background a vidiyo pompopompo
Limbikitsani kugwira ntchito mogwirizana pogwiritsa ntchito mawu ofotokoza zithunzi a AI
Onani data m'maganizo mwanu ndi matchati ochezera
Pezani tempuleti yanu yoyenera yopangira presentation
Pangani masilaidi mumasekondi ndi Magic Design
Pangani zithunzi ndi mavidiyo oyenda pogwiritsa ntchito ma effects otchuka
Pangani zithunzi zapamwamba zokongola zogwiritsa ntchito pa zopulinta
Pangani design komanso kupulinta pogwiritsa ntchito ma tempuleti a zantchito
Sinthani saizi ya ma design pompopompo kuti mugwiritse ntchito pa zopulinta zilizonse
Khazikikani pa brand ndi Brand Kit
Zipangizo zonse. Zonse zili pamodzi.
Kumanani ndi Visual Suite
Ndondomeko ya ntchito yanu yonse pa malo amodzi kuti mupange zinthu momasuka komanso kugwira ntchito limodzi, mothandizidwa ndi AI.
Onetsani mwamphamvu
Ganiziraninso ma presentation ndi zithunzi za m'makanema, kugwira ntchito limodzi mwaluntha, ndi zipangizo za AI.
Ma tempuleti ogwiritsa ntchito pa chilichonse
Pamayambiriro pa ma template
Pamapeto pa ma template